Mateyu 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Thetsa nkhani mofulumira ndi munthu wokuimba mlandu pamene ukupita naye kukhoti, kuti mwina wokuimba mlanduyo+ asakakupereke kwa woweruza. Komanso kuti woweruzayo asakakupereke kwa msilikali wa pakhoti kuti akuponye m’ndende. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:25 Nsanja ya Olonda,5/15/2008, ptsa. 6-7
25 “Thetsa nkhani mofulumira ndi munthu wokuimba mlandu pamene ukupita naye kukhoti, kuti mwina wokuimba mlanduyo+ asakakupereke kwa woweruza. Komanso kuti woweruzayo asakakupereke kwa msilikali wa pakhoti kuti akuponye m’ndende.