Mateyu 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ngati simukhululukira anthu machimo awo, Atate wanu sadzakukhululukirani machimo anu.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:15 Nsanja ya Olonda,2/1/2004, ptsa. 14-167/15/1996, tsa. 19