Mateyu 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwachitsanzo, chapafupi n’chiti, kunena kuti, Machimo ako akhululukidwa, kapena kunena kuti, Nyamuka uyende?+
5 Mwachitsanzo, chapafupi n’chiti, kunena kuti, Machimo ako akhululukidwa, kapena kunena kuti, Nyamuka uyende?+