Mateyu 13:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Choncho anayamba kukhumudwa naye.+ Koma Yesu anawauza kuti: “Mneneri salemekezedwa kwawo kapena m’nyumba mwake, koma kwina.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:57 Yesu—Ndi Njira, tsa. 121 Nsanja ya Olonda,7/1/1987, tsa. 8
57 Choncho anayamba kukhumudwa naye.+ Koma Yesu anawauza kuti: “Mneneri salemekezedwa kwawo kapena m’nyumba mwake, koma kwina.”+