Mateyu 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano Yesu atatsiriza mawu amenewa, anachoka ku Galileya ndi kubwera kumadera a kumalire kwa Yudeya kutsidya la Yorodano.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:1 Yesu—Ndi Njira, tsa. 222 Nsanja ya Olonda,7/15/1989, tsa. 8
19 Tsopano Yesu atatsiriza mawu amenewa, anachoka ku Galileya ndi kubwera kumadera a kumalire kwa Yudeya kutsidya la Yorodano.+