Maliko 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atachoka kumeneko anakafika kumadera a kumalire kwa Yudeya kutsidya la Yorodano. Kumenekonso khamu la anthu linasonkhananso kwa iye, ndipo mwachizolowezi chake anayamba kuwaphunzitsa.+ Yohane 10:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Chotero anawolokanso Yorodano ndi kupita kumene Yohane anali kubatizira+ poyamba, ndipo anakhala kumeneko.
10 Atachoka kumeneko anakafika kumadera a kumalire kwa Yudeya kutsidya la Yorodano. Kumenekonso khamu la anthu linasonkhananso kwa iye, ndipo mwachizolowezi chake anayamba kuwaphunzitsa.+
40 Chotero anawolokanso Yorodano ndi kupita kumene Yohane anali kubatizira+ poyamba, ndipo anakhala kumeneko.