Mateyu 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamapeto pake, pafupifupi 5 koloko madzulo* anapitanso ndipo anakapeza ena atangoimaima. Iye anawafunsa kuti, ‘N’chifukwa chiyani mwangoimaima pano tsiku lonse osagwira ntchito?’ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:6 Yesu—Ndi Njira, tsa. 226 Nsanja ya Olonda,8/15/1989, ptsa. 8-9
6 Pamapeto pake, pafupifupi 5 koloko madzulo* anapitanso ndipo anakapeza ena atangoimaima. Iye anawafunsa kuti, ‘N’chifukwa chiyani mwangoimaima pano tsiku lonse osagwira ntchito?’