Mateyu 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Madzulowo,+ mwinimunda wa mpesa uja anauza kapitawo wake kuti, ‘Itana antchito aja uwapatse malipiro awo,+ kuyambira omalizira, kutsiriza ndi oyambirira.’ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:8 Nsanja ya Olonda,8/15/1989, tsa. 8
8 “Madzulowo,+ mwinimunda wa mpesa uja anauza kapitawo wake kuti, ‘Itana antchito aja uwapatse malipiro awo,+ kuyambira omalizira, kutsiriza ndi oyambirira.’