Oweruza 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Patapita nthawi, mwamuna wina wokalamba anatulukira madzulowo+ akuchokera ku ntchito yake ya kumunda. Kwawo kwa mwamunayo kunali kudera lamapiri la Efuraimu,+ ndipo anali kukhala ku Gibeya kwa kanthawi, koma amuna a mumzindawo anali Abenjamini.+
16 Patapita nthawi, mwamuna wina wokalamba anatulukira madzulowo+ akuchokera ku ntchito yake ya kumunda. Kwawo kwa mwamunayo kunali kudera lamapiri la Efuraimu,+ ndipo anali kukhala ku Gibeya kwa kanthawi, koma amuna a mumzindawo anali Abenjamini.+