Mateyu 20:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno amuna awiri akhungu anakhala pansi m’mphepete mwa msewu ndipo atamva kuti Yesu akudutsa, anafuula kuti: “Ambuye, Mwana wa Davide, tichitireni chifundo!”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:30 Yesu—Ndi Njira, tsa. 230 Nsanja ya Olonda,9/15/1989, tsa. 82/1/1988, tsa. 5
30 Ndiyeno amuna awiri akhungu anakhala pansi m’mphepete mwa msewu ndipo atamva kuti Yesu akudutsa, anafuula kuti: “Ambuye, Mwana wa Davide, tichitireni chifundo!”+