Mateyu 26:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye anati: “Pitani mumzinda kwa Munthu wakutiwakuti+ ndipo mukamuuze kuti, Mphunzitsi wanena kuti, ‘Nthawi yanga yoikidwiratu yayandikira. Ndidzachita phwando la pasika pamodzi ndi ophunzira anga kunyumba kwako.’”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:18 Yesu—Ndi Njira, tsa. 267 Nsanja ya Olonda,8/1/2013, tsa. 106/1/1990, tsa. 9
18 Iye anati: “Pitani mumzinda kwa Munthu wakutiwakuti+ ndipo mukamuuze kuti, Mphunzitsi wanena kuti, ‘Nthawi yanga yoikidwiratu yayandikira. Ndidzachita phwando la pasika pamodzi ndi ophunzira anga kunyumba kwako.’”+