Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 21:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Wina aliyense akakakufunsani chilichonse, mukanene kuti, ‘Ambuye akuwafuna.’ Ndipo nthawi yomweyo akawatumiza kuno.”

  • Maliko 14:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pamenepo Yesu anatuma awiri mwa ophunzira akewo ndi kuwauza kuti: “Pitani mumzinda, ndipo mwamuna wina wosenza mtsuko wa madzi akakumana nanu.+ Mukam’tsatire ameneyo,

  • Luka 22:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iye anawayankha kuti:+ “Mukalowa mumzinda, mwamuna wina wosenza mtsuko wa madzi akumana nanu. Mukamutsatire kunyumba imene akalowe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena