Mateyu 26:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye anati: “Pitani mumzinda kwa Munthu wakutiwakuti+ ndipo mukamuuze kuti, Mphunzitsi wanena kuti, ‘Nthawi yanga yoikidwiratu yayandikira. Ndidzachita phwando la pasika pamodzi ndi ophunzira anga kunyumba kwako.’”+ Maliko 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Yesu anatuma awiri mwa ophunzira akewo ndi kuwauza kuti: “Pitani mumzinda, ndipo mwamuna wina wosenza mtsuko wa madzi akakumana nanu.+ Mukam’tsatire ameneyo,
18 Iye anati: “Pitani mumzinda kwa Munthu wakutiwakuti+ ndipo mukamuuze kuti, Mphunzitsi wanena kuti, ‘Nthawi yanga yoikidwiratu yayandikira. Ndidzachita phwando la pasika pamodzi ndi ophunzira anga kunyumba kwako.’”+
13 Pamenepo Yesu anatuma awiri mwa ophunzira akewo ndi kuwauza kuti: “Pitani mumzinda, ndipo mwamuna wina wosenza mtsuko wa madzi akakumana nanu.+ Mukam’tsatire ameneyo,