Maliko 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pamenepo iye anapita kumene kunali mayiyo n’kumuimiritsa, atamugwira dzanja. Atatero malungowo anatheratu+ moti mayiyo anayamba kuwatumikira.+
31 Pamenepo iye anapita kumene kunali mayiyo n’kumuimiritsa, atamugwira dzanja. Atatero malungowo anatheratu+ moti mayiyo anayamba kuwatumikira.+