Mateyu 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho anagwira dzanja la mayiwo,+ ndipo malungowo anatheratu, moti anadzuka n’kuyamba kumutumikira.+ Luka 4:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Chotero anaima pamene mayiwo anagona ndi kuwachiritsa,+ ndipo malungowo anatheratu. Nthawi yomweyo mayiwo anadzuka n’kuyamba kuwatumikira.+
15 Choncho anagwira dzanja la mayiwo,+ ndipo malungowo anatheratu, moti anadzuka n’kuyamba kumutumikira.+
39 Chotero anaima pamene mayiwo anagona ndi kuwachiritsa,+ ndipo malungowo anatheratu. Nthawi yomweyo mayiwo anadzuka n’kuyamba kuwatumikira.+