Mateyu 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho anagwira dzanja la mayiwo,+ ndipo malungowo anatheratu, moti anadzuka n’kuyamba kumutumikira.+ Maliko 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pamenepo iye anapita kumene kunali mayiyo n’kumuimiritsa, atamugwira dzanja. Atatero malungowo anatheratu+ moti mayiyo anayamba kuwatumikira.+
15 Choncho anagwira dzanja la mayiwo,+ ndipo malungowo anatheratu, moti anadzuka n’kuyamba kumutumikira.+
31 Pamenepo iye anapita kumene kunali mayiyo n’kumuimiritsa, atamugwira dzanja. Atatero malungowo anatheratu+ moti mayiyo anayamba kuwatumikira.+