Maliko 5:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndiyeno anagwira dzanja la mwanayo ndi kunena kuti: “Talʹi·tha cuʹmi,” mawu amene powamasulira amatanthauza kuti: “Kamtsikana iwe, ndikunena ndi iwe, Dzuka!”+ Machitidwe 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atatero anamugwira dzanja lake lamanja+ ndi kumuimiritsa. Nthawi yomweyo kunsi kwa mapazi ake komanso mafupa ake a akakolo zinalimba.+
41 Ndiyeno anagwira dzanja la mwanayo ndi kunena kuti: “Talʹi·tha cuʹmi,” mawu amene powamasulira amatanthauza kuti: “Kamtsikana iwe, ndikunena ndi iwe, Dzuka!”+
7 Atatero anamugwira dzanja lake lamanja+ ndi kumuimiritsa. Nthawi yomweyo kunsi kwa mapazi ake komanso mafupa ake a akakolo zinalimba.+