Mateyu 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Atatulutsa anthu aja panja, iye analowa ndi kugwira dzanja la mtsikanayo,+ ndipo iye anadzuka.+ Luka 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsiku linanso la sabata,+ iye analowa m’sunagoge n’kuyamba kuphunzitsa. Mmenemo munali munthu amene dzanja lake lamanja linali lopuwala.+
6 Tsiku linanso la sabata,+ iye analowa m’sunagoge n’kuyamba kuphunzitsa. Mmenemo munali munthu amene dzanja lake lamanja linali lopuwala.+