Mateyu 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho anagwira dzanja la mayiwo,+ ndipo malungowo anatheratu, moti anadzuka n’kuyamba kumutumikira.+ Yohane 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yesu anati: “Nyamuka, nyamula machira akowa ndi kuyamba kuyenda.”+ Machitidwe 9:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndiyeno Petulo anamuuza kuti:+ “Eneya, Yesu Khristu akukuchiritsa.+ Dzuka ndi kuyala bwino bedi lakoli.” Nthawi yomweyo anadzuka. Machitidwe 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho Paulo analankhula mokweza mawu kuti: “Imirira ndi miyendo yako!” Pamenepo iye anadumpha n’kuyamba kuyenda.+
15 Choncho anagwira dzanja la mayiwo,+ ndipo malungowo anatheratu, moti anadzuka n’kuyamba kumutumikira.+
34 Ndiyeno Petulo anamuuza kuti:+ “Eneya, Yesu Khristu akukuchiritsa.+ Dzuka ndi kuyala bwino bedi lakoli.” Nthawi yomweyo anadzuka.
10 Choncho Paulo analankhula mokweza mawu kuti: “Imirira ndi miyendo yako!” Pamenepo iye anadumpha n’kuyamba kuyenda.+