Machitidwe 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma Petulo anati: “Siliva ndi golide ndilibe, koma ndikupatsa chimene ndili nacho:+ M’dzina la Yesu Khristu Mnazareti,+ yenda!”+ Machitidwe 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 dziwani nonsenu ndi Aisiraeli onse, kuti m’dzina la Yesu Khristu Mnazareti+ uja, amene inu munamupachika pamtengo,+ koma amene Mulungu anamuukitsa kwa akufa,+ kudzera mwa iyeyo, munthu uyu waimirira pamaso panu atachira bwinobwino.
6 Koma Petulo anati: “Siliva ndi golide ndilibe, koma ndikupatsa chimene ndili nacho:+ M’dzina la Yesu Khristu Mnazareti,+ yenda!”+
10 dziwani nonsenu ndi Aisiraeli onse, kuti m’dzina la Yesu Khristu Mnazareti+ uja, amene inu munamupachika pamtengo,+ koma amene Mulungu anamuukitsa kwa akufa,+ kudzera mwa iyeyo, munthu uyu waimirira pamaso panu atachira bwinobwino.