Maliko 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Asaduki amene amanena kuti kulibe kuuka kwa akufa, anabwera kwa iye ndipo anam’funsa kuti:+
18 Kenako Asaduki amene amanena kuti kulibe kuuka kwa akufa, anabwera kwa iye ndipo anam’funsa kuti:+