Mateyu 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pa tsikulo Asaduki, amene amanena kuti kulibe kuuka kwa akufa, anabwera kwa iye n’kumufunsa kuti:+ Luka 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Asaduki ena, amene amanena kuti kulibe kuuka kwa akufa anafika+ ndi kuyamba kumufunsa, Machitidwe 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti Asaduki+ amanena kuti akufa sadzauka,+ kulibe angelo, kapena cholengedwa chauzimu, koma Afarisi amavomereza poyera kuti zonsezi zilipo.
23 Pa tsikulo Asaduki, amene amanena kuti kulibe kuuka kwa akufa, anabwera kwa iye n’kumufunsa kuti:+
8 Pakuti Asaduki+ amanena kuti akufa sadzauka,+ kulibe angelo, kapena cholengedwa chauzimu, koma Afarisi amavomereza poyera kuti zonsezi zilipo.