Maliko 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Asaduki amene amanena kuti kulibe kuuka kwa akufa, anabwera kwa iye ndipo anam’funsa kuti:+ Luka 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Asaduki ena, amene amanena kuti kulibe kuuka kwa akufa anafika+ ndi kuyamba kumufunsa, Machitidwe 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo anali okwiya chifukwa atumwiwo anali kuphunzitsa anthu ndi kulalikira mosapita m’mbali za kuuka kwa akufa pogwiritsa ntchito chitsanzo cha Yesu.+ Machitidwe 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti Asaduki+ amanena kuti akufa sadzauka,+ kulibe angelo, kapena cholengedwa chauzimu, koma Afarisi amavomereza poyera kuti zonsezi zilipo.
18 Kenako Asaduki amene amanena kuti kulibe kuuka kwa akufa, anabwera kwa iye ndipo anam’funsa kuti:+
2 Iwo anali okwiya chifukwa atumwiwo anali kuphunzitsa anthu ndi kulalikira mosapita m’mbali za kuuka kwa akufa pogwiritsa ntchito chitsanzo cha Yesu.+
8 Pakuti Asaduki+ amanena kuti akufa sadzauka,+ kulibe angelo, kapena cholengedwa chauzimu, koma Afarisi amavomereza poyera kuti zonsezi zilipo.