Luka 1:80 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Choncho mwana uja anakulirakulira+ ndipo anali kulimba mwauzimu. Iye anali kukhala m’zipululu mpaka tsiku lakuti adzionetsere poyera kwa Isiraeli. 1. Kuwala Kwenikweni kwa Dziko Malifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu Ulosi wa Zekariya (gnj 1 27:15–30:56)
80 Choncho mwana uja anakulirakulira+ ndipo anali kulimba mwauzimu. Iye anali kukhala m’zipululu mpaka tsiku lakuti adzionetsere poyera kwa Isiraeli.