Luka 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Yesu anawafunsa kuti: “Ndikufunseni anthu inu, Kodi malamulo amalola kuchita chiti pa sabata? Chabwino kapena choipa?+ Kupulumutsa moyo kapena kuuwononga?”+
9 Pamenepo Yesu anawafunsa kuti: “Ndikufunseni anthu inu, Kodi malamulo amalola kuchita chiti pa sabata? Chabwino kapena choipa?+ Kupulumutsa moyo kapena kuuwononga?”+