Mateyu 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma iye anawayankha kuti: “Ndani wa inu amene atakhala ndi nkhosa imodzi, ndiyeno nkhosayo n’kugwera m’dzenje+ tsiku la sabata, sangaigwire ndi kuitulutsa?+ Yohane 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ngati munthu amadulidwa tsiku la sabata posafuna kuphwanya chilamulo cha Mose, kodi mukundipsera mtima ine chifukwa ndinachiritsa munthu tsiku la sabata?+
11 Koma iye anawayankha kuti: “Ndani wa inu amene atakhala ndi nkhosa imodzi, ndiyeno nkhosayo n’kugwera m’dzenje+ tsiku la sabata, sangaigwire ndi kuitulutsa?+
23 Ngati munthu amadulidwa tsiku la sabata posafuna kuphwanya chilamulo cha Mose, kodi mukundipsera mtima ine chifukwa ndinachiritsa munthu tsiku la sabata?+