Luka 8:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Pamenepo, makolo akewo anakondwa kwambiri, koma Yesu anawalangiza kuti asauze aliyense zimene zachitikazo.+
56 Pamenepo, makolo akewo anakondwa kwambiri, koma Yesu anawalangiza kuti asauze aliyense zimene zachitikazo.+