Luka 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anawauza kuti: “Musanyamule kanthu pa ulendowu, musatenge ndodo, kapena thumba la chakudya, kapena mkate, kapena ndalama zasiliva, kapena kutenga malaya awiri amkati.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:3 Nsanja ya Olonda,3/15/2011, tsa. 67/15/1987, tsa. 27
3 Iye anawauza kuti: “Musanyamule kanthu pa ulendowu, musatenge ndodo, kapena thumba la chakudya, kapena mkate, kapena ndalama zasiliva, kapena kutenga malaya awiri amkati.+