Luka 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma iye anawayankha kuti: “Inuyo muwapatse chakudya.”+ Iwo anati: “Tilibe chilichonse kuno koma mitanda ya mkate isanu ndi nsomba+ ziwiri zokha basi. Mwina tingapite kukagula chakudya chokwanira anthu onsewa.”+
13 Koma iye anawayankha kuti: “Inuyo muwapatse chakudya.”+ Iwo anati: “Tilibe chilichonse kuno koma mitanda ya mkate isanu ndi nsomba+ ziwiri zokha basi. Mwina tingapite kukagula chakudya chokwanira anthu onsewa.”+