Luka 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Patapita masiku pafupifupi 8 chinenereni mawu amenewa, iye anatenga Petulo, Yohane ndi Yakobo ndi kukwera nawo m’phiri kukapemphera.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:28 Nsanja ya Olonda,3/15/2008, tsa. 319/15/1991, tsa. 21
28 Patapita masiku pafupifupi 8 chinenereni mawu amenewa, iye anatenga Petulo, Yohane ndi Yakobo ndi kukwera nawo m’phiri kukapemphera.+