Luka 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho khalani m’nyumba yamtendereyo.+ Muzidya ndi kumwa zimene angakupatseni,+ chifukwa wantchito ayenera kulandira malipiro ake.+ Musamachoke kumene mwafikirako n’kupita kunyumba zina.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:7 Galamukani!,4/8/1994, ptsa. 14-19
7 Choncho khalani m’nyumba yamtendereyo.+ Muzidya ndi kumwa zimene angakupatseni,+ chifukwa wantchito ayenera kulandira malipiro ake.+ Musamachoke kumene mwafikirako n’kupita kunyumba zina.+