-
Luka 11:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako anawauza kuti: “Ndani wa inu amene ali ndi bwenzi lake kumene angapite pakati pa usiku kukam’pempha kuti, ‘Bwanawe, ndibwerekeko mitanda itatu ya mkate,
-