Luka 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Munthu akayatsa nyale saiika m’chipinda cha pansi kapena kuivundikira ndi dengu, koma amaiika pachoikapo nyale,+ kuti onse olowa aone kuwala. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:33 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 176-177 Nsanja ya Olonda,8/15/1988, ptsa. 8-9
33 Munthu akayatsa nyale saiika m’chipinda cha pansi kapena kuivundikira ndi dengu, koma amaiika pachoikapo nyale,+ kuti onse olowa aone kuwala.