Mateyu 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu akayatsa nyale, saivundikira ndi dengu,+ koma amaiika pachoikapo nyale ndipo imaunikira onse m’nyumbamo. Maliko 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano anapitiriza kuwauza kuti: “Nyale saivundikira ndi dengu loyezera zinthu kapena kuiika pansi pa bedi, amatero kodi? Koma amaiika pachoikapo nyale, si choncho kodi?+ Luka 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Palibe amene amati akayatsa nyale, amaivundikira ndi chiwiya kapena kuiika pansi pa bedi. Koma amaiika pachoikapo nyale kuti amene akulowa aone kuwala.+
15 Anthu akayatsa nyale, saivundikira ndi dengu,+ koma amaiika pachoikapo nyale ndipo imaunikira onse m’nyumbamo.
21 Tsopano anapitiriza kuwauza kuti: “Nyale saivundikira ndi dengu loyezera zinthu kapena kuiika pansi pa bedi, amatero kodi? Koma amaiika pachoikapo nyale, si choncho kodi?+
16 “Palibe amene amati akayatsa nyale, amaivundikira ndi chiwiya kapena kuiika pansi pa bedi. Koma amaiika pachoikapo nyale kuti amene akulowa aone kuwala.+