Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Anthu akayatsa nyale, saivundikira ndi dengu,+ koma amaiika pachoikapo nyale ndipo imaunikira onse m’nyumbamo.

  • Maliko 4:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Tsopano anapitiriza kuwauza kuti: “Nyale saivundikira ndi dengu loyezera zinthu kapena kuiika pansi pa bedi, amatero kodi? Koma amaiika pachoikapo nyale, si choncho kodi?+

  • Luka 11:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Munthu akayatsa nyale saiika m’chipinda cha pansi kapena kuivundikira ndi dengu, koma amaiika pachoikapo nyale,+ kuti onse olowa aone kuwala.

  • Afilipi 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 kuti mukhale opanda chifukwa chokunenezani nacho ndiponso osalakwa.+ Mukhale ana a Mulungu opanda chilema+ pakati pa m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota,+ umene mukuwala pakati pawo monga zounikira m’dzikoli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena