Luka 19:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Poyankha iye anati: “Ndithu ndikukuuzani, ngati awa atakhala chete, miyala+ ingathe kufuula.”