-
Yohane 1:48Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
48 Natanayeli anati: “Mwandidziwa bwanji?” Yesu anamuyankha kuti: “Filipo asanakuitane, ine ndinakuona, muja unali pansi pa mkuyu paja.”
-