Yohane 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho anafika mumzinda wa Samariya wotchedwa Sukari pafupi ndi munda umene Yakobo anapatsa mwana wake Yosefe.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:5 Nsanja ya Olonda,2/1/1997, tsa. 30
5 Choncho anafika mumzinda wa Samariya wotchedwa Sukari pafupi ndi munda umene Yakobo anapatsa mwana wake Yosefe.+