Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 33:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kenako anagula malo ndipo anamangapo msasa. Anawagula ndi ndalama zasiliva 100, kwa ana a Hamori, bambo wake wa Sekemu.+

  • Genesis 48:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Koma ine ndikukuwonjezera gawo limodzi la dziko kuposa abale ako,+ limene ndinalanda Aamori ndi lupanga langa ndi uta wanga.”

  • Yoswa 24:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Mafupa a Yosefe,+ amene ana a Isiraeli anabweretsa kuchokera ku Iguputo anawaika m’manda ku Sekemu, pamalo amene Yakobo anagula kwa ana a Hamori,+ tate wa Sekemu. Malowo anawagula ndi ndalama zasiliva zokwana 100,+ ndipo anakhala a ana a Yosefe monga cholowa chawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena