Machitidwe 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako mafupa awo anawatengera ku Sekemu,+ kumene anakawaika m’manda.+ Anawaika m’manda amene Abulahamu anagula ndi ndalama zasiliva kwa ana a Hamori mu Sekemu.+
16 Kenako mafupa awo anawatengera ku Sekemu,+ kumene anakawaika m’manda.+ Anawaika m’manda amene Abulahamu anagula ndi ndalama zasiliva kwa ana a Hamori mu Sekemu.+