Yohane 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Filipo anamuyankha kuti: “Ngakhale mitanda ya mkate ya ndalama zokwana madinari 200 singawakwanire amenewa. Singawakwanire ngakhale titati aliyense angolandirako pang’ono.”+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:7 Yesu—Ndi Njira, tsa. 128 Nsanja ya Olonda,9/1/1987, ptsa. 16-17
7 Filipo anamuyankha kuti: “Ngakhale mitanda ya mkate ya ndalama zokwana madinari 200 singawakwanire amenewa. Singawakwanire ngakhale titati aliyense angolandirako pang’ono.”+