Yohane 6:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Pamenepo ambiri mwa ophunzira ake atamva zimenezi anati: “Mawu amenewa ndi ozunguza. Ndani angamvetsere zimenezi?”+
60 Pamenepo ambiri mwa ophunzira ake atamva zimenezi anati: “Mawu amenewa ndi ozunguza. Ndani angamvetsere zimenezi?”+