Yohane 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu waganyu,+ amene si m’busa ndipo nkhosazo si zake, akaona mmbulu ukubwera amasiya nkhosazo ndi kuthawa, pamenepo mmbuluwo umazigwira ndi kuzibalalitsa,+
12 Munthu waganyu,+ amene si m’busa ndipo nkhosazo si zake, akaona mmbulu ukubwera amasiya nkhosazo ndi kuthawa, pamenepo mmbuluwo umazigwira ndi kuzibalalitsa,+