Yohane 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chimene Atate+ wanga wandipatsa n’chofunika kuposa zinthu zonse,+ ndipo palibe amene angazitsomphole m’dzanja la Atate.+
29 Chimene Atate+ wanga wandipatsa n’chofunika kuposa zinthu zonse,+ ndipo palibe amene angazitsomphole m’dzanja la Atate.+