Yohane 10:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 nanga kodi inu mukundiuza ine woyeretsedwa ndi Atate ndi kutumizidwa m’dziko kuti, ‘Ukunyoza Mulungu,’ chifukwa ndanena kuti, Ndine Mwana wa Mulungu?+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:36 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 188-189 Nsanja ya Olonda,11/15/1988, tsa. 9
36 nanga kodi inu mukundiuza ine woyeretsedwa ndi Atate ndi kutumizidwa m’dziko kuti, ‘Ukunyoza Mulungu,’ chifukwa ndanena kuti, Ndine Mwana wa Mulungu?+