Yohane 11:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Inde, ndikudziwa kuti mumandimva nthawi zonse, koma ndikunena izi chifukwa cha khamu la anthu+ aimirira panowa, kuti akhulupirire kuti inu munandituma ine.”+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:42 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 214-215 Nsanja ya Olonda,5/15/1989, tsa. 8
42 Inde, ndikudziwa kuti mumandimva nthawi zonse, koma ndikunena izi chifukwa cha khamu la anthu+ aimirira panowa, kuti akhulupirire kuti inu munandituma ine.”+