-
Yohane 11:51Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
51 Zimene ananenazi, kwenikweni sanaziganize mwa iye yekha, koma chifukwa anali mkulu wa ansembe chaka chimenecho, ananenera kuti Yesu adzafera mtunduwo.
-