Yohane 11:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Pa chifukwa chimenechi, Yesu sanalinso kuyendayenda moonekera+ kwa Ayuda.+ Koma anachoka kumeneko ndi kupita kudera lina lapafupi ndi chipululu, mumzinda wotchedwa Efuraimu.+ Ndipo anakhala kumeneko pamodzi ndi ophunzira ake. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:54 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 215-216 Nsanja ya Olonda,6/1/1989, tsa. 85/15/1989, tsa. 9
54 Pa chifukwa chimenechi, Yesu sanalinso kuyendayenda moonekera+ kwa Ayuda.+ Koma anachoka kumeneko ndi kupita kudera lina lapafupi ndi chipululu, mumzinda wotchedwa Efuraimu.+ Ndipo anakhala kumeneko pamodzi ndi ophunzira ake.