Yohane 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso chilichonse chimene mudzapemphe m’dzina langa, ine ndidzachichita, kuti Atate alemekezedwe mwa Mwana wake.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:13 Nsanja ya Olonda,8/1/1990, tsa. 8
13 Komanso chilichonse chimene mudzapemphe m’dzina langa, ine ndidzachichita, kuti Atate alemekezedwe mwa Mwana wake.+