Yohane 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndithudi ndikukuuzani, Mudzagwetsa misozi ndi kulira mofuula, koma dzikoli lidzasangalala. Mudzamva chisoni,+ koma chisoni chanu adzachisandutsa chimwemwe.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:20 Yesu—Ndi Njira, tsa. 278 Nsanja ya Olonda,9/1/1990, ptsa. 8-9
20 Ndithudi ndikukuuzani, Mudzagwetsa misozi ndi kulira mofuula, koma dzikoli lidzasangalala. Mudzamva chisoni,+ koma chisoni chanu adzachisandutsa chimwemwe.+